NKHANI
-
SUKULU YA MZUNI YATSEKEDWA
Sukulu ya ukachenjede ya mzuni yatsekedwa kutsatila zionetselo zomwe zinachitika dzulo Kamba kakusakondwa ndi kukwera kwa ndalama yolipilira maphunziro awo.…
Read More » -
NTHAMBI ZOMWE SIZABOMA AZIYAMIKIRA PONTHANDINZA ANTHU OMWE ADAKHUDZIDWA NDI NAMONDWE
Wolemba : Precious Kalino. Atsogoleri akale a dziko lino Dr Bakili Muluzi ndi Dr Joyce Banda ayamikila nthambi zomwe sizaboma…
Read More » -
BUNGWE LA CHRR LATI ANTHU MDZIKO MUNO AKUYENERA KUKHALA NDI CHIDWI PA NTCHITO YOPENZA MAUNTHENGA MOSABVUTA
Bungwe la Center for Human Rights and Rehabilitation CHRR lati anthu mdziko muno akuyenela kukhala ndi chidwi pogwilitsa ntchito lamulo…
Read More » -
BUNGWE LA LILONGWE WATER BOARD LALIMBIKITSA ACHINYAMATA KUTENGAPO GAWO PA NTCHITO YOSAMALILA MALO WOCHITIPO MALONDA.
Achinyamata omwe amagwila ntchito Bungwe logawa madzi mu nzinda wa Lilongwe anakonza mwambo okonza depot ya Lilongwe komanso malo ena…
Read More » -
MTSOGOLERI WA DZIKO LINO LAZARUS CHAKWERA WATSIMIKIZILA A MALAWI KUTI MKUMANO WA ATSOGOLELI AMAYIKO WA NUMBER 78 UBWELETSA MAYANKHO PAMAVUTO ENA OMWE AKHUDZA DZIKO LINO.
Wolemba : Pemphero Phiri. Mtsogoleli wadziko lino Lazarus Chakwera watsimikizila a Malawi kuti mkumano wa atsogoleli amayiko wa number 78…
Read More » -
DZIKO LA NIGERIA LAKHUDZIDWA NDI VUTO LAMAGETSI
Dziko la Nigeria la khudzidwa ndi bvuto la magetsi potsatira kusokonekera kwa makina awo omwe amanthandinzira kuperekera magetsi . Makampani…
Read More » -
UNDUNA WA ZACHILENGEDWE WAPEREKA NTHANDINZO LA NSOMBA ZOKWANA MA TANI 1.8 KU CHIPATALA CHA KCH
Unduna woona zachilengedwe komanso kusintha kwa nyengo dzulo wapeleka thandizo la nsomba zokwana ma tani 1.8 ku chipatala cha Kamuzu…
Read More » -
BOMA LATI PALI KUFUNIKIRA KOTUKULA NTCHITO ZA MAKONO ZA ICT M’SUKULU ZONSE KUPHATIKIZAPO SUKULU ZA PULAIMALE M’DZIKO MUNO.
Wolemba : Angela Mwape. Boma lati pali kufunikira kotukula ntchito za makono za ICT m’sukulu zonse kuphatikizapo sukulu za pulaimale…
Read More » -
AKATSWIRI PA NTCHITO ZAMAPHUNZIRO ATI BOMA LIKUYENERA KUWUNIKANSO NDONDOMEKO ZOMWE LIMAGWIRITSA NTCHITO
Wolemba : Tionge Longwe. Kusowekela kwa mankhalidwe abwino komaso kudzipeleke kwa aphuzitsi ndi ophuzila ati ndi komwe kwachititsa kuti sukulu…
Read More » -
BUNGWE LOYANGANILA MATENDA A TB NDI KHATE LASAKHA MAYI WA PFUKO KUKHALA MTSOGOLERI PA NTCHITO YONTHANA NDI NTHENDA YA TB MDZIKO MUNO.
Bungwe lomwe likuyendetsa ndondomeko yofuna kuthana ndi nthenda yachifuwa chachikulu komanso khate la National TB and Leprosy Elimination Program (NTLEP)…
Read More »