NKHANI
Boma lasintha chiganizo chomwe chinalipo pochotsa ndalama zomwe adakodza kuti zigwire ntchito kuchoka pa 244 milion kufika 50 million kwacha.

Wolemba :Blessings Makuwira
Boma lasintha chiganizo chomwe chinalipo pochotsa ndalama zomwe adakodza kuti zigwire ntchito kuchoka pa 244 milion kufika 50 million kwacha.
Polankhula ndi olemba nkhani wathu wa CRS ku Lilongwe, chairperson koma omwe akuyendetsa mwambowu yemweso ndi nduna ya za dziko a Richard Chimwemwe Banda ati dongosolo lomwe linalipo kuti ku Mzuzu, Lilongwe koma Blantyre kuti kukhala chisangalalochi ati ku Lilongwe konkha ndkomwe kuzakhale chisangalalochi chomwe chizachitike nd mapephelo onkha.
Pameneposo boma lati anthu omwe axaloleledwe kulowa ndi ikwana 200 onkha komaso omwe ayitanidwa ku chiwoneselochi.