NKHANI

BUNGWE LA CHRR LATI ANTHU MDZIKO MUNO AKUYENERA KUKHALA NDI CHIDWI PA NTCHITO YOPENZA MAUNTHENGA MOSABVUTA

Bungwe la Center for Human Rights and Rehabilitation CHRR lati anthu mdziko muno
akuyenela kukhala ndi chidwi pogwilitsa ntchito lamulo lopeza mauthenga mosavuta.

Mmodzi mwa akulu akulu ku bungweli Denis Mwafulirwa ndiye wanena izi lachisanu pa
mkumano ndi atenga mbali osiyana siyana mboma la Salima pofuna kuwadziwitsa zakufunikila
kongwilitsa ntchito lamuloli.

Mwafulirwa wapemphaso mabungwe omwe si aboma kuti achilimikike pofalitsa mauthenga
okhudza lamuloli ndikufunikila kwake pochita zinthu poyela mboma.

Pakadali pano mkhala pa mpando wa mngwilizano wa mabungwe omwe si aboma mboma la
Salima Paul Dancun wati pali kufowoka pakangwilitsidwe ntchito ka lamuloli koma wati
mkumanowu uwapatsaso chidwi chofuna kufunsa mauthenga ofunikila ku boma.

Tags
Show More

Related Articles

Back to top button
Close
Close