NKHANI

BUNGWE LA LILONGWE WATER BOARD LALIMBIKITSA ACHINYAMATA KUTENGAPO GAWO PA NTCHITO YOSAMALILA MALO WOCHITIPO MALONDA.

Achinyamata omwe amagwila ntchito Bungwe logawa madzi mu nzinda wa Lilongwe anakonza mwambo okonza depot ya Lilongwe komanso malo ena oyandikana ndi depoyiti.

Malingana ndi mtsogoleri wa achinyamatawa, Ashley win Mandele wati ntchitoyi ndi mbali imodzi yoonetsetsa kuti anthu akusitha ndikuchita ukhondo mu nzindawu komanso madela ena
uzungulira.

Mandala anapitiliza kupempha achinyamata kutengapo gawo posamalila malo ochitila malonda
osiyanasiyana ndicholinga chothana ndi matenda omwe amadza Kamba kakusowa kwa
ukhondo monga cholera.

Tags
Show More

Related Articles

Back to top button
Close
Close