NKHANI

CHIWERENGERO CHA ANTHU OMWALIRA A TIMU YA NYUNGWE FC CHAFIKA PA 25

Bungwe lomwe limayan’anira masewero a mpira wamiyendo m’dziko muno la Football association of Malawi (FAM) lati chiwelengero cha anthu omwalira kutimu ya Nyungwe FC chakwera kufika pa 25.
Malinga ndi bungweli chiwerengerochi chakwera pakutsatira kwa imfa potsatira ya m’modzi mwa anyamata omwe amasewera mu timu yi, Gaula Nyirenda yemwe amalandira thandizo kuchipatala china chigawo chakumpoto.
Nyirenda akhale a kulowa m’manda lero (lachitatu).
Timu ya Nyungwe inachita ngozi ya galimoto pomwe imachokera kusewera masewero awo a Northern Region Moto Division One nditimu ya Chitipa Hammers loweruka lapitali.
Source :Fam.
Tags
Show More

Related Articles

Back to top button
Close
Close