NKHANI

Kampani ya Dwangwa Sugar yapeleka nthandinzo ku Police y Khunga

Wolemba Innocent Chunga

Company yopanga shuga ku Dwangwa yapeleka thandizo la zogwilira ntchito ku police ya Nkhunga m’boma la Nkhotakota.

Polankhura pamwambo opeleka thandizoli mkulu wa company ya Illovo ku Dwangwa A Jerry Ndlovu adati mchitidwe wa umbava ndilomwe lakhala vuto ku company yawo ndipo zikuonetsa kuti mbamvazi ndizozungulira company yawo.

Tags
Show More

Related Articles

Back to top button
Close
Close