NKHANI

Katswiri pa nkhani za maphunziro wayamikila m’gwilizano omwe ulipo pakati pa dziko la united kingdom ndi dziko la Malawi

Wolemba Tapiwa Mbewe 

Katswiri pa nkhani za maphunziro wayamikila m’gwilizano omwe ulipo pakati pa dziko la united kingdom ndi dziko la Malawi pofuna kutukula maphuziro a mwana wamkazi.

Poyakhula ndi wailesi ya Chisomo, Katswiri pa maphunziro Lucky Mbewe wati gwilizanowu uthandiza  kutukula  maphunziro a atsikana m’dziko.

Padakali pano;Wachiwiri kwa mtsogoleri wadziko lino yemwe ndi nduna yowona ndondomeko zachuma ndi chitukuko cha dziko ndi chitukuko Dr Lazarus Chakwera wayamikira Dr Chakwera popelereka mfundo zothyakuka ku mkumanowu zotulukula dziko lino pfuna kukwaniritsa masomphenya a mchaka cha 2063 “Agenda 2063” mchingerezi.

Tags
Show More

Related Articles

Back to top button
Close
Close