NKHANI

M’thambi yowona za ngozi zogwa mwadzidzi ya DoDMA yati yafikira mawanja pafupifupi 94 pa 100 aliwonse

Wolemba :Brian Chigumula Jnr.

M’thambi yowona za ngozi zogwa mwadzidzi ya DoDMA yati yafikira mawanja pafupifupi 94 pa 100 aliwonse omwe anakhudzidwa ndi ngozi zogwa mwadzidzidzi kuchokera mmwezi wa July chaka chatha kufikira mwezi wa July chaka chino.

Mkulu woyang’anira zathandizo losiyanasiyana ku nthambiyi Ephold Kachigwada wati nthambi yawo yafikira mawanja okwana 35,077 ndi thandizo pa mawanja 37,132 omwe anakhudzidwa ndi ngozizi.

Tags
Show More

Related Articles

Back to top button
Close
Close