NKHANI

Zokonzekera Mwambo omwe umakhalapo chaka ndi chaka wa Lake of Stars zili mchimake ku salima

Gulu la anthu a mabungwe osiyanasiyana linakumana loweluka ku senga-bay m’boma la salima komwe amasesa mu dera la nzindawu kuyambira pansika wa senga-bay kukamalizira ku kabumba rodge ngati njira imodzi yokonzekera mwambo wa lake of stars omwe udzachitikire kukambumba rodge kuyambira pa 28 mpaka pa 30 september chaka chino.

Poyankhula ndi wailesi ya chisomo womwe anakonza mwambo wosesawu yemwe ndi wankulu wa Safali Rodge a Iven Dosantas anati cholinga chosesa mu derali nkufuna kulimbikitsa ukhondo makamaka kwa anthu amene amangotaya zinyalala palipose.

Mmawu ake yemwe akuyimilira mwambo wa lake of stars a Shamirah Elias anati anachiona kuti ndichanzeru kukonza mu m’derali kaamba ndicholinga chofuna kuphunzitsa anthu ena kuti kutaila zinyalala palipose kumabweretsa matenga.

Show More

Related Articles

Leave a Reply

Back to top button
Close
Close